Miyambo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kudzakupulumutsanso kwa anthu amene amasangalala kuchita zoipa,+ amene amakondwera ndi zinthu zoipa ndi zopotoka,+ 1 Akorinto 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sichikondwera ndi zosalungama,+ koma chimakondwera ndi choonadi.+
14 Kudzakupulumutsanso kwa anthu amene amasangalala kuchita zoipa,+ amene amakondwera ndi zinthu zoipa ndi zopotoka,+