Salimo 50:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi zonse ukaona wakuba unali kusangalala naye.+Ndipo unali kugwirizana ndi anthu achigololo.+ Hoseya 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo amasangalatsa mfumu ndi zoipa zawo, ndiponso amasangalatsa akalonga ndi chinyengo chawo.+ Luka 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anakondwa, ndipo anagwirizana kuti amupatse ndalama zasiliva.+ Aroma 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Amenewa ngakhale kuti amalidziwa bwino lamulo lolungama la Mulungu,+ lakuti amene amachita zinthu zimenezi n’ngoyenera imfa,+ iwo amapitiriza kuzichita. Kuwonjezera apo, amagwirizananso+ ndi anthu amene amachita zimenezo.
32 Amenewa ngakhale kuti amalidziwa bwino lamulo lolungama la Mulungu,+ lakuti amene amachita zinthu zimenezi n’ngoyenera imfa,+ iwo amapitiriza kuzichita. Kuwonjezera apo, amagwirizananso+ ndi anthu amene amachita zimenezo.