Yesaya 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma iyenso ndi wanzeru ndipo adzabweretsa tsoka,Komanso sadzabweza mawu ake. Iye adzaukira nyumba ya anthu ochita zoipaKomanso amene amathandiza anthu ochita zoipa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:2 Yesaya 1, ptsa. 319-320
2 Koma iyenso ndi wanzeru ndipo adzabweretsa tsoka,Komanso sadzabweza mawu ake. Iye adzaukira nyumba ya anthu ochita zoipaKomanso amene amathandiza anthu ochita zoipa.+