Yesaya 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iyenso ndi wanzeru+ ndipo adzabweretsa tsoka.+ Sadzabweza mawu ake+ ndipo adzaukira nyumba ya anthu ochita zoipa.+ Adzalepheretsa anthu amene amachita zopweteka anzawo, kupeza chithandizo chimene amafuna.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:2 Yesaya 1, ptsa. 319-320
2 Iyenso ndi wanzeru+ ndipo adzabweretsa tsoka.+ Sadzabweza mawu ake+ ndipo adzaukira nyumba ya anthu ochita zoipa.+ Adzalepheretsa anthu amene amachita zopweteka anzawo, kupeza chithandizo chimene amafuna.+