Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Esau analinso kutchedwa Edomu.+ Deuteronomo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Auze anthuwo kuti: “Mukudutsa m’malire a dziko la abale anu,+ ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri.+ Iwo adzachita nanu mantha,+ choncho muyenera kukhala osamala kwambiri. Deuteronomo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Usaipidwe ndi Mwedomu, chifukwa ndi m’bale wako.+ “Usaipidwe ndi Mwiguputo, chifukwa unali mlendo m’dziko lawo.+
4 Auze anthuwo kuti: “Mukudutsa m’malire a dziko la abale anu,+ ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri.+ Iwo adzachita nanu mantha,+ choncho muyenera kukhala osamala kwambiri.
7 “Usaipidwe ndi Mwedomu, chifukwa ndi m’bale wako.+ “Usaipidwe ndi Mwiguputo, chifukwa unali mlendo m’dziko lawo.+