Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Esau analinso kutchedwa Edomu.+ Numeri 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsiku lina Mose anatumiza amithenga kuchokera ku Kadesi kumene iwo anali, kupita kwa mfumu ya Edomu,+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene ationekera ife.+ Deuteronomo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Usaipidwe ndi Mwedomu, chifukwa ndi m’bale wako.+ “Usaipidwe ndi Mwiguputo, chifukwa unali mlendo m’dziko lawo.+
14 Tsiku lina Mose anatumiza amithenga kuchokera ku Kadesi kumene iwo anali, kupita kwa mfumu ya Edomu,+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene ationekera ife.+
7 “Usaipidwe ndi Mwedomu, chifukwa ndi m’bale wako.+ “Usaipidwe ndi Mwiguputo, chifukwa unali mlendo m’dziko lawo.+