Ekisodo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo mafumu a ku Edomu adzasokonezeka.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera ndi mantha.+Ndithu, anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+ Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+ Deuteronomo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Lero ndichititsa anthu a mitundu ina okhala pansi pa thambo, amene adzamva za inu, kuchita nanu mantha kwambiri ndi kuyamba kukuopani. Chifukwa cha inu, iwo adzanthunthumira ndi kumva zopweteka zofanana ndi zowawa za pobereka.’+
15 Pamenepo mafumu a ku Edomu adzasokonezeka.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera ndi mantha.+Ndithu, anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+
27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+
25 Lero ndichititsa anthu a mitundu ina okhala pansi pa thambo, amene adzamva za inu, kuchita nanu mantha kwambiri ndi kuyamba kukuopani. Chifukwa cha inu, iwo adzanthunthumira ndi kumva zopweteka zofanana ndi zowawa za pobereka.’+