Genesis 27:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma Isaki bambo ake anamuuza kuti: “Taona, udzakhala kutali ndi nthaka yachonde, kotalikirana ndi mame akumwamba.+ Genesis 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano nayi mibadwo ya Esau, kholo la Aedomu, amene anali kukhala kudera lamapiri la Seiri.+ Deuteronomo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero tinalambalala abale athu, ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba,+ Elati ndi Ezioni-geberi.+ “Kenako tinatembenuka ndi kudutsa njira ya m’chipululu cha Mowabu.+
39 Koma Isaki bambo ake anamuuza kuti: “Taona, udzakhala kutali ndi nthaka yachonde, kotalikirana ndi mame akumwamba.+
8 Chotero tinalambalala abale athu, ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba,+ Elati ndi Ezioni-geberi.+ “Kenako tinatembenuka ndi kudutsa njira ya m’chipululu cha Mowabu.+