Genesis 27:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Udzakhalira moyo lupanga+ ndipo udzatumikira m’bale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa m’khosi mwako.”+ Genesis 36:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mayina a ana a Esau ndi awa: Elifazi, mwana wamwamuna wobadwa kwa Ada mkazi wake wa Esau, komanso Reueli, mwana wamwamuna wobadwa kwa Basemati mkazi wake wa Esau.+
40 Udzakhalira moyo lupanga+ ndipo udzatumikira m’bale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa m’khosi mwako.”+
10 Mayina a ana a Esau ndi awa: Elifazi, mwana wamwamuna wobadwa kwa Ada mkazi wake wa Esau, komanso Reueli, mwana wamwamuna wobadwa kwa Basemati mkazi wake wa Esau.+