Mlaliki 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndinadzipangira minda yokongola ndi malo obzalamo maluwa ndi mitengo.+ Mmenemu ndinabzalamo mitengo ya zipatso zosiyanasiyana. Nyimbo ya Solomo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Wachikondi wanga watsetserekera kumunda wake,+ kumabedi am’munda a maluwa onunkhira,+ kuti akadyetse ziweto+ kuminda, ndiponso kuti akathyole maluwa.
5 Ndinadzipangira minda yokongola ndi malo obzalamo maluwa ndi mitengo.+ Mmenemu ndinabzalamo mitengo ya zipatso zosiyanasiyana.
2 “Wachikondi wanga watsetserekera kumunda wake,+ kumabedi am’munda a maluwa onunkhira,+ kuti akadyetse ziweto+ kuminda, ndiponso kuti akathyole maluwa.