Nyimbo ya Solomo 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tiye tilawirire m’mawa tipite kuminda ya mpesa. Tikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira,+ ngati yatuluka maluwa,+ ndiponso ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.+ Kumeneko ndikakusonyeza chikondi changa.+
12 Tiye tilawirire m’mawa tipite kuminda ya mpesa. Tikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira,+ ngati yatuluka maluwa,+ ndiponso ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.+ Kumeneko ndikakusonyeza chikondi changa.+