Nyimbo ya Solomo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nditenge,+ tiye tithawe! Chifukwatu mfumu yandipititsa m’zipinda zake zamkati.+ Tiye tikondwere ndi kusangalalira limodzi. Tiye tinene za chikondi chimene umandisonyeza osati za vinyo.+ M’pake kuti atsikana amakukonda.+ Nyimbo ya Solomo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chikondi chimene umandisonyeza n’chokoma,+ iwe mlongo wanga, mkwatibwi wanga. Chikondi chimene umandisonyeza n’chabwino kuposa vinyo ndipo kununkhira kwa mafuta ako odzola n’koposa zonunkhira za mitundu yonse.+
4 Nditenge,+ tiye tithawe! Chifukwatu mfumu yandipititsa m’zipinda zake zamkati.+ Tiye tikondwere ndi kusangalalira limodzi. Tiye tinene za chikondi chimene umandisonyeza osati za vinyo.+ M’pake kuti atsikana amakukonda.+
10 Chikondi chimene umandisonyeza n’chokoma,+ iwe mlongo wanga, mkwatibwi wanga. Chikondi chimene umandisonyeza n’chabwino kuposa vinyo ndipo kununkhira kwa mafuta ako odzola n’koposa zonunkhira za mitundu yonse.+