Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mtsikana aliyense anali kukaonekera kwa Mfumu Ahasiwero pambuyo poti am’chitira zonse zimene amayenera kum’chitira pa miyezi 12 malinga ndi lamulo lokhudza akazi. Atsikanawo anali kuwapaka mafuta a mule*+ miyezi 6 kenako anali kuwapaka mafuta a basamu+ pamodzi ndi mafuta enanso okongoletsa miyezi inanso 6. Akachita zimenezi ndiye kuti amaliza dongosolo lonse lowakongoletsera.

  • Nyimbo ya Solomo 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mafuta+ ako odzola ndi onunkhira bwino. Dzina lako lili ngati mafuta othira pamutu.+ N’chifukwa chake atsikana amakukonda.

  • Nyimbo ya Solomo 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Pamene mfumu yakhala patebulo lake lozungulira, fungo labwino la nado*+ wanga likumveka kwa wokondedwa wanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena