Miyambo 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndawaza pabedi panga zonunkhiritsa za mule, aloye ndi sinamoni.+ Nyimbo ya Solomo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi n’chiyani, chooneka ngati utsi wokwera m’mwamba, chonunkhira mafuta a mule, lubani,*+ ndi mtundu uliwonse wa zonunkhira za ufa za munthu wamalonda?”+ Luka 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma mayi wina amene anali wodziwika mumzindawo kuti ndi wochimwa, anamva kuti Yesu akudya chakudya m’nyumba ya Mfarisi. Choncho anapita komweko ndi botolo lopangidwa ndi mwala wa alabasitala,+ muli mafuta onunkhira.
6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi n’chiyani, chooneka ngati utsi wokwera m’mwamba, chonunkhira mafuta a mule, lubani,*+ ndi mtundu uliwonse wa zonunkhira za ufa za munthu wamalonda?”+
37 Koma mayi wina amene anali wodziwika mumzindawo kuti ndi wochimwa, anamva kuti Yesu akudya chakudya m’nyumba ya Mfarisi. Choncho anapita komweko ndi botolo lopangidwa ndi mwala wa alabasitala,+ muli mafuta onunkhira.