Ekisodo 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Koma iweyo utenge mafuta awa onunkhira, abwino koposa:+ madontho oundana a mule*+ masekeli 500, sinamoni*+ wonunkhira bwino hafu ya muyezo wa mule, kapena kuti masekeli 250, ndi kalamasi* wonunkhira+ wokwana masekeli 250. Ekisodo 30:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Tenga zonunkhira izi:+ madontho a sitakate,* onika, mafuta onunkhira a galibanamu ndi lubani*+ weniweni. Zonsezi zikhale za muyezo wofanana.
23 “Koma iweyo utenge mafuta awa onunkhira, abwino koposa:+ madontho oundana a mule*+ masekeli 500, sinamoni*+ wonunkhira bwino hafu ya muyezo wa mule, kapena kuti masekeli 250, ndi kalamasi* wonunkhira+ wokwana masekeli 250.
34 Ndiyeno Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Tenga zonunkhira izi:+ madontho a sitakate,* onika, mafuta onunkhira a galibanamu ndi lubani*+ weniweni. Zonsezi zikhale za muyezo wofanana.