Nyimbo ya Solomo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi n’chiyani, chooneka ngati utsi wokwera m’mwamba, chonunkhira mafuta a mule, lubani,*+ ndi mtundu uliwonse wa zonunkhira za ufa za munthu wamalonda?”+ Nyimbo ya Solomo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 maluwa a safironi,+ mabango onunkhira,+ sinamoni,+ komanso mitengo yosiyanasiyana ya lubani, mule, aloye,+ ndi zonunkhira zonse zabwino kwambiri.+
6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi n’chiyani, chooneka ngati utsi wokwera m’mwamba, chonunkhira mafuta a mule, lubani,*+ ndi mtundu uliwonse wa zonunkhira za ufa za munthu wamalonda?”+
14 maluwa a safironi,+ mabango onunkhira,+ sinamoni,+ komanso mitengo yosiyanasiyana ya lubani, mule, aloye,+ ndi zonunkhira zonse zabwino kwambiri.+