Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 43:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno bambo awo Isiraeli anawauza kuti: “Chabwino, ngati ndi choncho,+ chitani izi: Tengani zinthu zamtengo wapatali za dziko lino m’matumba anu, mukam’patse munthuyo monga mphatso.+ Tengani mafuta a basamu+ pang’ono, uchi+ pang’ono, mafuta onunkhira a labidanamu, khungwa la utomoni wonunkhira,+ mtedza wa pisitasho, ndi zipatso za amondi.+

  • 1 Mafumu 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mfumukaziyo inafika ku Yerusalemu ndi anthu ambiri oiperekeza.+ Inabwera ndi ngamila+ zitanyamula mafuta a basamu,+ golide wambiri, ndi miyala yamtengo wapatali. Inafika kwa Solomo n’kuyamba kunena zonse zimene zinali kumtima kwake.+

  • 2 Mafumu 20:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Hezekiya anawamvetsera anthuwo ndipo anawaonetsa zonse za m’nyumba yake yosungiramo chuma.+ Anawaonetsa siliva, golide,+ mafuta a basamu,+ mafuta abwino, nyumba yake yosungiramo zida zankhondo, ndi chuma chake chonse. Palibe chimene Hezekiya sanawaonetse m’nyumba yake ndi mu ufumu wake wonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena