Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 mafuta a nyale,+ mafuta a basamu+ opangira mafuta odzozera,+ ndi zofukiza zonunkhira.+

  • Esitere 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mtsikana aliyense anali kukaonekera kwa Mfumu Ahasiwero pambuyo poti am’chitira zonse zimene amayenera kum’chitira pa miyezi 12 malinga ndi lamulo lokhudza akazi. Atsikanawo anali kuwapaka mafuta a mule*+ miyezi 6 kenako anali kuwapaka mafuta a basamu+ pamodzi ndi mafuta enanso okongoletsa miyezi inanso 6. Akachita zimenezi ndiye kuti amaliza dongosolo lonse lowakongoletsera.

  • Yeremiya 8:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi mu Giliyadi+ mulibe mafuta a basamu? Kapena kodi mulibe wochiritsa mmenemo?+ N’chifukwa chiyani nanga mwana wamkazi wa anthu anga sakuchira?+

  • Yeremiya 46:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Iwe namwali, mwana wamkazi wa Iguputo,+ pita ku Giliyadi kuti ukatenge mafuta a basamu.+ Wachulukitsa njira zochiritsira zosathandiza koma sudzachiritsidwa.+

  • Ezekieli 27:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘“Unali kuchita malonda ndi Yuda komanso dziko la Isiraeli. Unapereka zinthu zimene unasunga posinthanitsa+ ndi tirigu+ wa ku Miniti,+ zakudya zapamwamba, uchi,+ mafuta ndi basamu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena