Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 58:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Mukatero kuwala kwanu kudzaonekera ngati m’bandakucha,+ ndipo mudzachira mofulumira kwambiri.+ Chilungamo chanu chizidzayenda patsogolo panu,+ ndipo ulemerero wa Yehova uzidzalondera kumbuyo kwanu.+

  • Yeremiya 30:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yehova wanena kuti: “Sudzachira kuvulala kwako.+ Chilonda chako cha mkwapulo ndi chosachiritsika.+

  • Yeremiya 30:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Ndidzakubwezeretsa mwakale ndipo ndidzachiritsa zilonda zako za mkwapulo,”+ watero Yehova. “Iwo anakutcha kuti mkazi wothamangitsidwa ndipo anali kunena kuti:+ ‘Ameneyu ndi Ziyoni ndipo palibe amene akumufunafuna.’”+

  • Yeremiya 33:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye wanena kuti: ‘Ine ndichiritsa anthu a mumzindawu ndi kuwapatsa thanzi labwino.+ Ndiwachiritsa ndi kuwapatsa mtendere wochuluka ndi choonadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena