Yeremiya 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 N’chifukwa chiyani zopweteka zanga sizikutha+ ndiponso chilonda changa cha mkwapulo sichikupola?+ Chilondacho sichikumva mankhwala. Inu Mulungu, mwakhala ngati kasupe wosachedwa kuuma,+ ndiponso ngati mtsinje wosadalirika.+
18 N’chifukwa chiyani zopweteka zanga sizikutha+ ndiponso chilonda changa cha mkwapulo sichikupola?+ Chilondacho sichikumva mankhwala. Inu Mulungu, mwakhala ngati kasupe wosachedwa kuuma,+ ndiponso ngati mtsinje wosadalirika.+