Yeremiya 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’chifukwa chiyani ukulira pamene wadzivulaza mwadala?+ Ululu wako ndi wosachiritsika chifukwa zolakwa zako zachuluka ndipo machimo ako ndi ochuluka kwambiri.+ Ine ndakuchitira zimenezi.
15 N’chifukwa chiyani ukulira pamene wadzivulaza mwadala?+ Ululu wako ndi wosachiritsika chifukwa zolakwa zako zachuluka ndipo machimo ako ndi ochuluka kwambiri.+ Ine ndakuchitira zimenezi.