Yesaya 57:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ine ndaona njira zake. Ndinayamba kumuchiritsa+ ndi kumutsogolera,+ ndiponso ndinamutonthoza+ iyeyo ndi anthu ake amene anali kulira.”+
18 Ine ndaona njira zake. Ndinayamba kumuchiritsa+ ndi kumutsogolera,+ ndiponso ndinamutonthoza+ iyeyo ndi anthu ake amene anali kulira.”+