Yeremiya 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Bwererani, inu ana opanduka.+ Ndidzachiritsa kusakhulupirika kwanu.”+ “Ife tabwerera! Tabwera kwa inu, pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+ Yeremiya 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye wanena kuti: ‘Ine ndichiritsa anthu a mumzindawu ndi kuwapatsa thanzi labwino.+ Ndiwachiritsa ndi kuwapatsa mtendere wochuluka ndi choonadi.+ Hoseya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ndidzathetsa kusakhulupirika kwawo.+ Ndidzawakonda mwa kufuna kwanga,+ chifukwa mkwiyo wanga wawachokera.+
22 “Bwererani, inu ana opanduka.+ Ndidzachiritsa kusakhulupirika kwanu.”+ “Ife tabwerera! Tabwera kwa inu, pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+
6 Iye wanena kuti: ‘Ine ndichiritsa anthu a mumzindawu ndi kuwapatsa thanzi labwino.+ Ndiwachiritsa ndi kuwapatsa mtendere wochuluka ndi choonadi.+
4 “Ndidzathetsa kusakhulupirika kwawo.+ Ndidzawakonda mwa kufuna kwanga,+ chifukwa mkwiyo wanga wawachokera.+