Deuteronomo 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Sikuti Yehova anakusonyezani chikondi ndi kukusankhani chifukwa chakuti munali ochuluka kuposa mitundu yonse,+ chifukwatu mtundu wanu unali waung’ono mwa mitundu yonse.+ Zefaniya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova Mulungu wako ali pakati pa anthu ako ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu.+ Iye adzakondwera nawe.+ Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza, ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe.
7 “Sikuti Yehova anakusonyezani chikondi ndi kukusankhani chifukwa chakuti munali ochuluka kuposa mitundu yonse,+ chifukwatu mtundu wanu unali waung’ono mwa mitundu yonse.+
17 Yehova Mulungu wako ali pakati pa anthu ako ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu.+ Iye adzakondwera nawe.+ Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza, ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe.