Salimo 78:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma anawamvera chifundo.+ Anali kukhululukira* machimo awo+ ndipo sanali kuwawononga.+Nthawi zambiri anali kubweza mkwiyo wake,+Ndipo sanali kuwasonyeza ukali wake wonse. Yesaya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+
38 Koma anawamvera chifundo.+ Anali kukhululukira* machimo awo+ ndipo sanali kuwawononga.+Nthawi zambiri anali kubweza mkwiyo wake,+Ndipo sanali kuwasonyeza ukali wake wonse.
12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+