Ekisodo 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno mngelo+ wa Mulungu woona amene anali kuyenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka n’kupita kumbuyo kwawo. Motero, mtambo woima njo ngati chipilala uja unachoka kutsogolo n’kukaima kumbuyo kwawo.+ Yesaya 52:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu inu simudzatuluka mwachipwirikiti, komanso simudzachoka chothawa.+ Pakuti Yehova azidzayenda patsogolo panu,+ ndipo Mulungu wa Isiraeli azidzalondera kumbuyo kwanu.+
19 Ndiyeno mngelo+ wa Mulungu woona amene anali kuyenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka n’kupita kumbuyo kwawo. Motero, mtambo woima njo ngati chipilala uja unachoka kutsogolo n’kukaima kumbuyo kwawo.+
12 Anthu inu simudzatuluka mwachipwirikiti, komanso simudzachoka chothawa.+ Pakuti Yehova azidzayenda patsogolo panu,+ ndipo Mulungu wa Isiraeli azidzalondera kumbuyo kwanu.+