Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 102:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Inu mudzanyamuka ndi kusonyeza Ziyoni chifundo,+

      Pakuti imeneyi ndi nyengo yomukomera mtima,

      Chifukwa nthawi yoikidwiratu yakwana.+

  • Salimo 103:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Tamanda amene akukukhululukira zolakwa zako zonse,+

      Iye amene akukuchiritsa matenda ako onse.+

  • Yeremiya 33:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye wanena kuti: ‘Ine ndichiritsa anthu a mumzindawu ndi kuwapatsa thanzi labwino.+ Ndiwachiritsa ndi kuwapatsa mtendere wochuluka ndi choonadi.+

  • Hoseya 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Bwerani anthu inu. Tiyeni tibwerere kwa Yehova,+ pakuti iye watikhadzulakhadzula+ koma adzatichiritsa.+ Wakhala akutivulaza koma adzamanga zilonda zathu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena