Salimo 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaonetsa poyera kulungama kwako kuti kuunike ngati kuwala,+Adzaonetsa poyera chilungamo chako kuti chiwale ngati usana.+ Salimo 112:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waunika mu mdima kuti anthu owongoka mtima aone kuwala.+ ח [Chehth]Iye ndi wachisomo, wachifundo ndi wolungama.+ Miyambo 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma njira ya olungama ili ngati kuwala kwamphamvu kumene kumamka kuwonjezereka mpaka tsiku litakhazikika.+
6 Iye adzaonetsa poyera kulungama kwako kuti kuunike ngati kuwala,+Adzaonetsa poyera chilungamo chako kuti chiwale ngati usana.+
4 Waunika mu mdima kuti anthu owongoka mtima aone kuwala.+ ח [Chehth]Iye ndi wachisomo, wachifundo ndi wolungama.+
18 Koma njira ya olungama ili ngati kuwala kwamphamvu kumene kumamka kuwonjezereka mpaka tsiku litakhazikika.+