Yeremiya 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe amene akuchonderera kuti chilonda chako chipole.+ Palibe njira iliyonse yokuchiritsira ndipo palibe mankhwala amene angakuthandize.+
13 Palibe amene akuchonderera kuti chilonda chako chipole.+ Palibe njira iliyonse yokuchiritsira ndipo palibe mankhwala amene angakuthandize.+