Yeremiya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi mu Giliyadi+ mulibe mafuta a basamu? Kapena kodi mulibe wochiritsa mmenemo?+ N’chifukwa chiyani nanga mwana wamkazi wa anthu anga sakuchira?+
22 Kodi mu Giliyadi+ mulibe mafuta a basamu? Kapena kodi mulibe wochiritsa mmenemo?+ N’chifukwa chiyani nanga mwana wamkazi wa anthu anga sakuchira?+