Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 32:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Hezekiya anakhala ndi chuma chambiri ndi ulemerero wochuluka zedi.+ Anadzimangira nyumba zosungiramo siliva, golide,+ miyala yamtengo wapatali,+ mafuta a basamu,+ zishango,+ ndi zinthu zonse zabwinozabwino.+

  • Salimo 49:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Anthu amene akukhulupirira chuma chawo,+

      Amene akudzitamandira chifukwa cha kuchuluka kwa chuma chawo,+

  • Yeremiya 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitamande chifukwa cha nzeru zake.+ Munthu wamphamvu asadzitamande chifukwa cha mphamvu zake.+ Munthu wachuma asadzitamande chifukwa cha chuma chake.”+

  • Yakobo 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma tsopano mumakonda kudzitama.+ Kunyada konse koteroko ndi koipa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena