Salimo 52:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu wamphamvu wotere sadalira Mulungu monga malo ake achitetezo,+Koma amadalira kuchuluka kwa chuma chake,+Ndipo chitetezo chake amachipeza m’mavuto amene iyeyo amawachititsa.+ Yesaya 47:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwe unali kudalira zoipa zako.+ Wanena kuti: “Palibe amene akundiona.”+ Wasochera chifukwa cha nzeru zako ndiponso chifukwa chodziwa zinthu.+ Mumtima mwako umakhalira kunena kuti: “Ndine ndekha, palibenso wina.”
7 Munthu wamphamvu wotere sadalira Mulungu monga malo ake achitetezo,+Koma amadalira kuchuluka kwa chuma chake,+Ndipo chitetezo chake amachipeza m’mavuto amene iyeyo amawachititsa.+
10 Iwe unali kudalira zoipa zako.+ Wanena kuti: “Palibe amene akundiona.”+ Wasochera chifukwa cha nzeru zako ndiponso chifukwa chodziwa zinthu.+ Mumtima mwako umakhalira kunena kuti: “Ndine ndekha, palibenso wina.”