Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 49:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti amaona kuti ngakhale anthu anzeru amafa,+

      Wopusa ndi wopanda nzeru, onsewo amawonongeka,+

      Ndipo chuma chawo amasiyira anthu ena.+

  • Miyambo 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse,+ ndipo usadalire luso lako lomvetsa zinthu.+

  • Mlaliki 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nditaganizanso ndinaona kuti padziko lapansi pano anthu othamanga kwambiri sapambana pampikisano,+ amphamvu sapambana pankhondo,+ anzeru sapeza chakudya,+ omvetsa zinthu nawonso sapeza chuma,+ ndipo ngakhale odziwa zinthu sakondedwa,+ chifukwa nthawi yatsoka ndi zinthu zosayembekezereka zimagwera onsewo.+

  • Yesaya 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsoka kwa amene amadziona ngati anzeru komanso amadziyesa ochenjera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena