Yeremiya 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Munthu waliwiro ndi munthu wamphamvu asayese dala kuthawa.+ Iwo apunthwa ndi kugwa.+ Zimenezi zachitikira kumpoto+ m’mphepete mwa mtsinje wa Firate.’ Amosi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+
6 ‘Munthu waliwiro ndi munthu wamphamvu asayese dala kuthawa.+ Iwo apunthwa ndi kugwa.+ Zimenezi zachitikira kumpoto+ m’mphepete mwa mtsinje wa Firate.’
14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+