2 Mafumu 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mfumu ya Iguputo sinatulukenso+ m’dziko lake,+ chifukwa mfumu ya Babulo inali itatenga zinthu zonse zomwe zinali za mfumu ya Iguputo,+ kuyambira kuchigwa*+ cha Iguputo kukafika kumtsinje wa Firate.+ Yesaya 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu ambiri pakati pawo adzapunthwa n’kugwa ndi kuthyoka, ndipo adzakodwa n’kugwidwa.+
7 Mfumu ya Iguputo sinatulukenso+ m’dziko lake,+ chifukwa mfumu ya Babulo inali itatenga zinthu zonse zomwe zinali za mfumu ya Iguputo,+ kuyambira kuchigwa*+ cha Iguputo kukafika kumtsinje wa Firate.+