Genesis 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+ Numeri 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno malirewo akalowere kuchigwa* cha Iguputo+ mpaka kukafika ku Nyanja Yaikulu.+ Yoswa 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anapitirira kukafika ku Azimoni+ mpaka kuchigwa cha Iguputo,+ n’kukathera kunyanja. Amenewa ndiwo anali malire awo a kum’mwera.
18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+
4 Ndiyeno anapitirira kukafika ku Azimoni+ mpaka kuchigwa cha Iguputo,+ n’kukathera kunyanja. Amenewa ndiwo anali malire awo a kum’mwera.