Yoswa 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anapitirira kukafika ku Azimoni+ mpaka kuchigwa cha Iguputo+ nʼkukathera ku Nyanja.* Amenewa anali malire awo akumʼmwera.
4 Ndiyeno anapitirira kukafika ku Azimoni+ mpaka kuchigwa cha Iguputo+ nʼkukathera ku Nyanja.* Amenewa anali malire awo akumʼmwera.