Yoswa 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anapitirira kukafika ku Azimoni+ mpaka kuchigwa cha Iguputo,+ n’kukathera kunyanja. Amenewa ndiwo anali malire awo a kum’mwera.
4 Ndiyeno anapitirira kukafika ku Azimoni+ mpaka kuchigwa cha Iguputo,+ n’kukathera kunyanja. Amenewa ndiwo anali malire awo a kum’mwera.