Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 42:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma Yakobo sanalole kuti Benjamini,+ m’bale wake wa Yosefe, apite limodzi ndi abale akewo, chifukwa anati: “Mwina angakumane ndi tsoka n’kufa.”+

  • 1 Samueli 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno muonetsetse izi: Likasalo likadzalowera njira yopita kwawo, ku Beti-semesi,+ ndiye kuti iye ndi amenedi watichitira choipa chachikuluchi. Koma ngati sililowera kumeneko, tidziwa kuti si dzanja lake limene latikhudza, koma ngozi+ yangotigwera.”

  • 1 Mafumu 22:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ndiyeno munthu wina anakoka uta n’kuponya muvi wake chiponyeponye, koma analasa mfumu ya Isiraeli pampata umene unali pakati pa chovala chake chokhala ndi mamba achitsulo, ndi zovala zake zina zodzitetezera. Choncho mfumuyo inauza woyendetsa galeta lake kuti:+ “Tembenuza dzanja lako ndipo unditulutse m’bwalo lankhondoli, chifukwa ndavulala kwambiri.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena