Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kuchokera ku Baala, malirewo anazungulira chakumadzulo kulowera kuphiri la Seiri, n’kukadutsa pamalo otsetsereka a phiri la Yearimu kumpoto, kutanthauza Kesaloni. Ndiyeno anatsetserekera ku Beti-semesi,+ n’kukafika ku Timuna.+

  • Yoswa 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aini+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Yuta+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda 9, kuchokera m’mafuko awiri amenewa.

  • 2 Mafumu 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma Amaziya sanamvere.+

      Chotero Yehoasi, mfumu ya Isiraeli, anabwera, ndipo iye ndi Amaziya mfumu ya Yuda anamenyana+ ku Beti-semesi+ m’dziko la Yuda.

  • 1 Mbiri 6:59
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 mzinda wa Asani+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto.

  • 2 Mbiri 28:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nawonso Afilisiti+ anaukira mizinda ya Yuda ya ku Sefela+ ndi ku Negebu+ n’kulanda mizinda ya Beti-semesi,+ Aijaloni,+ Gederoti,+ Soko+ ndi midzi yake yozungulira, Timuna+ ndi midzi yake yozungulira, komanso Gimizo ndi midzi yake yozungulira, n’kuyamba kukhala kumeneko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena