Yoswa 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aini+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Yuta+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda 9, kuchokera m’mafuko awiri amenewa. 1 Mbiri 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Midzi yawo inali Etami, Aini, Rimoni, Tokeni, ndi Asani.+ Mizinda isanu.
16 Aini+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Yuta+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda 9, kuchokera m’mafuko awiri amenewa.