Yoswa 15:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Libina,+ Eteri,+ Asani, Yoswa 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munalinso Aini,+ Rimoni,+ Eteri, ndi Asani.+ Mizinda inayi ndi midzi yake, 1 Mbiri 6:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 mzinda wa Asani+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto.
59 mzinda wa Asani+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Beti-semesi+ ndi malo ake odyetserako ziweto.