1 Samueli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Afilisiti anatenga likasa+ la Mulungu woona kuchoka nalo ku Ebenezeri n’kupita nalo ku Asidodi.+ 1 Samueli 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho, anthu okhala mumzinda wa Yabesi-giliyadi+ anamva zimene Afilisiti anamuchita Sauli. 2 Mbiri 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anapita kukamenyana ndi Afilisiti+ ndipo anagumula mpanda wa ku Gati,+ wa ku Yabine+ ndi wa ku Asidodi.+ Kenako anamanga mizinda m’chigawo cha Asidodi+ ndiponso pakati pa Afilisiti.
5 Tsopano Afilisiti anatenga likasa+ la Mulungu woona kuchoka nalo ku Ebenezeri n’kupita nalo ku Asidodi.+
6 Iye anapita kukamenyana ndi Afilisiti+ ndipo anagumula mpanda wa ku Gati,+ wa ku Yabine+ ndi wa ku Asidodi.+ Kenako anamanga mizinda m’chigawo cha Asidodi+ ndiponso pakati pa Afilisiti.