Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 19:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Eloni, Timuna,+ Ekironi,+

  • Oweruza 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako anapita kukauza bambo ndi mayi ake kuti: “Ine ndaona mkazi ku Timuna mwa ana aakazi a Afilisiti, choncho mukam’tenge kuti akhale mkazi wanga.”+

  • 2 Mbiri 28:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nawonso Afilisiti+ anaukira mizinda ya Yuda ya ku Sefela+ ndi ku Negebu+ n’kulanda mizinda ya Beti-semesi,+ Aijaloni,+ Gederoti,+ Soko+ ndi midzi yake yozungulira, Timuna+ ndi midzi yake yozungulira, komanso Gimizo ndi midzi yake yozungulira, n’kuyamba kukhala kumeneko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena