Genesis 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anakhalabe m’chipululu cha Parana,+ ndipo amayi ake anakamutengera mkazi kudziko la Iguputo. Genesis 34:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Potsirizira pake, Sekemu anauza bambo ake Hamori+ kuti: “Munditengere mtsikana ameneyu kuti akhale mkazi wanga.”+ Genesis 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Patapita nthawi, Yuda anatengera mkazi Ere, mwana wake woyamba. Mkaziyo dzina lake anali Tamara.+
4 Potsirizira pake, Sekemu anauza bambo ake Hamori+ kuti: “Munditengere mtsikana ameneyu kuti akhale mkazi wanga.”+