Genesis 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anakhalabe m’chipululu cha Parana,+ ndipo amayi ake anakamutengera mkazi kudziko la Iguputo. Oweruza 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anapita kukauza bambo ndi mayi ake kuti: “Ine ndaona mkazi ku Timuna mwa ana aakazi a Afilisiti, choncho mukam’tenge kuti akhale mkazi wanga.”+
2 Kenako anapita kukauza bambo ndi mayi ake kuti: “Ine ndaona mkazi ku Timuna mwa ana aakazi a Afilisiti, choncho mukam’tenge kuti akhale mkazi wanga.”+