Yoswa 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kuchokera ku Baala, malirewo anazungulira chakumadzulo kulowera kuphiri la Seiri, n’kukadutsa pamalo otsetsereka a phiri la Yearimu kumpoto, kutanthauza Kesaloni. Ndiyeno anatsetserekera ku Beti-semesi,+ n’kukafika ku Timuna.+ Oweruza 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Samisoni anapita ku Timuna+ ndipo kumeneko anaona mkazi mwa ana aakazi a Afilisiti.
10 Kuchokera ku Baala, malirewo anazungulira chakumadzulo kulowera kuphiri la Seiri, n’kukadutsa pamalo otsetsereka a phiri la Yearimu kumpoto, kutanthauza Kesaloni. Ndiyeno anatsetserekera ku Beti-semesi,+ n’kukafika ku Timuna.+