-
2 Mbiri 18:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Ndiyeno munthu wina anakoka uta n’kuponya muvi wake chiponyeponye, koma analasa+ mfumu ya Isiraeli pampata umene unali pakati pa chovala chake chokhala ndi mamba achitsulo, ndi zovala zake zina zodzitetezera. Choncho mfumuyo inauza woyendetsa galeta lake kuti:+ “Tembenuza galetali ndipo unditulutse m’bwalo lankhondoli, chifukwa ndavulala kwambiri.”+
-