2 Mbiri 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako asilikali oponya mivi+ analasa Mfumu Yosiya. Choncho mfumuyo inauza atumiki ake kuti: “Nditsitseni pakuti ndavulala kwambiri.”+ Salimo 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Masoka adzapha munthu woipa.+Ndipo wodana ndi munthu wolungama adzapezeka wolakwa.+
23 Kenako asilikali oponya mivi+ analasa Mfumu Yosiya. Choncho mfumuyo inauza atumiki ake kuti: “Nditsitseni pakuti ndavulala kwambiri.”+