Deuteronomo 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Samalani kuti munganene mumtima mwanu kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza ndi mphamvu zanga ndi nyonga za dzanja langa.’+ Salimo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+ Danieli 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+ 1 Akorinto 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero pasakhale munthu wodzitama chifukwa cha anthu, popeza zinthu zonse ndi zanu,+
17 Samalani kuti munganene mumtima mwanu kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza ndi mphamvu zanga ndi nyonga za dzanja langa.’+
16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+
30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+